Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.01 2
  • January 2-8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 2-8
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.01 2

January 2-8

2 MAFUMU 22-23

  • Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “N’chifukwa Chiyani Kudzichepetsa N’kwabwino?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mf 23:24, 25​—Kodi chitsanzo cha Yosiya chingalimbikitse bwanji anthu amene anakulira m’banja limene anthu ake ankachita zoipa? (w01-CN 4/15 26:3-4)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 23:16-23 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Pemphero​—Sl 65:2. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)

  • Ulendo Woyamba: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba, kenako yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01 la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 120

  • Kodi N’kudzichepetsa Kapena N’kudzikweza? (Yak 4:6): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi kudzichepetsa n’kosiyana bwanji ndi kudzikweza? Kodi tingaphunzire chiyani pa chitsanzo cha Mose? N’chifukwa chiyani muli wofunitsitsa kukhala wodzichepetsa?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 23

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani