Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.03 10
  • March 27–April 2

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 27–April 2
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.03 10

March 27–April 2

2 MBIRI 5-7

  • Nyimbo Na. 129 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 6:29, 30​—Kodi mawu otchulidwa mu pemphero la Solomowa angatilimbikitse bwanji? (w10-CN 12/1 11:7)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 6:28-35 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha zimene tinganene. Ngati mwininyumba wasonyeza chidwi yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Tizikumbukira Imfa ya Yesu, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pambuyo pa nkhani ya Chikumbutso, yambani kukambirana ndi munthu amene munamuitana ndipo muyankhe funso limene wafunsa lokhudza mwambowu. (th phunziro 17)

  • Nkhani: (5 min.) w93-CN 2/1 31​—Mutu: Kodi Tingatani Ngati Sitingakwanitse Kupezeka pa Chikumbutso pa Zifukwa Zina? (th phunziro 18)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 36

  • “Uteteze Mtima Wako”: (10 min.) Nkhani komanso vidiyo.

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff kubwereza gawo 2

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 54 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani