Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.07 20
  • Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Anthu Okhulupirika kwa Yehova Amakwaniritsa Zimene Alonjeza
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
  • Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Mukhoza Kutumikira Yehova Ngakhale Makolo Anu Si Chitsanzo Chabwino
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.07 20

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova

Mabanja anapemphedwa kuti asiye nyumba komanso malo awo n’kupita ku Yerusalemu (Ne 11:1; w98-CN 10/15 22:13)

Anthu omwe anasiya zinthu zimenezi anadalitsidwa (Ne 11:2; w86-CN 2/15 26)

Nthawi zonse madalitso ochokera kwa Yehova amakhala ochuluka kwambiri kuposa zinthu zimene tingasiye (Mki 3:10; w16-CN 04 8:15)

Zithunzi: 1. Banja likulongedza katundu wawo m’makatoni ndi m’chikwama. 2. Banja lomwe lija, lomwe likutumikira m’dziko lina, likulalikira mzimayi.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndapeza madalitso otani chifukwa cha zinthu zomwe ndinasiya pofuna kutumikira Yehova?’

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani