Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.09 18
  • Moyo Ukafika Povuta

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Moyo Ukafika Povuta
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • “Yembekezera Yehova”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2022
  • Kodi Yobu Anali Ndani?
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.09 18

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Moyo Ukafika Povuta

Pamene ankakumana ndi mayesero, Yobu anayerekezera moyo ndi ntchito yokakamiza (Yob 7:1; w06-CN 3/15 14:10)

Mavuto amene Yobu ankakumana nawo anam’chititsa kufotokoza momasuka mmene ankamvera (Yob 7:11)

Anafika mpaka ponena kuti akufuna kufa (Yob 7:16; w20.12 51:1)

M’bale wachinyamata ali kunyumba kwa mnzake wachikulire ndipo akufotokoza nkhawa zake.

Mukaona kuti moyo wanu wafika povuta kwambiri, muzipemphera kwa Yehova mochokera pansi pamtima, kumuuza zonse zomwe zili mumtima mwanu, komanso muzifotokozera mnzanu wodalirika mmene mukumvera. Imeneyi ikhoza kukhala njira yoyamba imene ingakuthandizeni kuti muyambenso kumva bwino.—g 1/12 16-17.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani