November 6-12
YOBU 13-14
Nyimbo Na. 151 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Munthu Akafa, Kodi Angakhalenso ndi Moyo?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 13:1-10 (th phunziro 12)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Baibulo—2Ti 3:16, 17. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 2)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff kubwereza gawo 1 funso 1-5 (phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muziika Kenakake Pambali”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo. Ikambidwe ndi mkulu. Yamikirani abale ndi alongo chifukwa choti amasunga ndalama zothandizira pa ntchito za Ufumu.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff 55:5, Zomwe Taphunzira, Kubwereza Komanso Zolinga
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 84 ndi Pemphero