November 13-19
YOBU 15-17
Nyimbo Na. 90 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Musamatsanzire Elifazi Potonthoza Ena”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yob 16:22—Kodi mawu amene Yobu analankhulawa akusonyeza kuti sankakhulupirira zoti akufa adzauka? (w06 3/15 14 ¶11)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 17:1-10 (th phunziro 12)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Baibulo—Yob 26:7. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mufotokozereni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 11)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff kubwereza gawo 1 funso 6-10 (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff 56:1-6 ndi Mawu Akumapeto 6, 7
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 101 ndi Pemphero