December 4-10
YOBU 22-24
Nyimbo Na. 49 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Munthu Angakhale Waphindu kwa Mulungu?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yob 23:13—Kodi kuganizira chitsanzo cha Yehova kungatithandize bwanji kukwaniritsa zolinga zauzimu? (w04 7/15 21-22)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 22:1-9 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 11)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo?, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 2)
Nkhani: (5 min.) w21.05 18-19 ¶17-20—Mutu: Kuona Zinthu Moyenera Kumachititsa Kuti Yehova Apitirize Kutigwiritsa Ntchito. (th phunziro 20)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Makolo, Muziphunzitsa Ana Anu Kudziwa Mmene Angasangalatsire Mulungu”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Zofunika Pampingo: (5 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff 59-1-5
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 55 ndi Pemphero