Magazini Yophunzira
JULY 2020
NKHANI ZOPHUNZIRA: AUGUST 31–SEPTEMBER 27, 2020
© 2020 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Davide sanaope kumenyana ndi Goliati ngakhale kuti anali wamng’ono ndipo ankaoneka ngati wopanda mphamvu. Iye anadalira Yehova kuti amupatse mphamvu zogonjetsera Goliati ndipo anamugonjetsadi (Onani nkhani yophunzira 29, ndime 11)