Magazini Yophunzira
DECEMBER 2020
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: FEBRUARY 1-28, 2021
© 2020 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Banja lina lomwe limakhala m’dziko limene ntchito yathu ndi yoletsedwa, likupitirizabe kuchita zinthu zonse zokhudza kulambira ndipo akukhulupirira kuti Mulungu adzakwaniritsa zinthu zabwino zomwe analonjeza (Onani nkhani yophunzira 50, ndime 4)