Magazini Yophunzira
DECEMBER 2021
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JANUARY 31–FEBRUARY 27, 2022
© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Mawu akuti “Chiyero n’cha Yehova” ankalembedwa pa kachitsulo kagolide komwe kankakhala panduwira ya mkulu wa ansembe (Onani nkhani yophunzira 48, ndime 6-7)