Magazini Yophunzira
JANUARY 2022
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: FEBRUARY 28–APRIL 3, 2022
© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
LEMBA LA CHAKA CHA 2022:
“Ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.”—SAL. 34:10
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Pa nthawi ya chisautso chachikulu, Gogi wa ku Magogi adzayesa kutiukira m’nyumba zathu. Koma sitidzachita mantha podziwa kuti Yesu ndi angelo ake akuona zomwe zikuchitika ndipo atiteteza (Onani nkhani yophunzira 1, ndime 13)