Magazini Yophunzira
JULY 2022
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: SEPTEMBER 5–OCTOBER 2, 2022
© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Mofanana ndi zidutswa za chithunzi zomwe zikaikidwa pamodzi chithunzicho chimaoneka bwinobwino, maulosi a Baibulo a m’mabuku a Danieli ndi Chivumbulutso amatithandiza kuona pomwe tili munthawi ya Yehova ya zochitika zosiyanasiyana (Onani nkhani yophunzira 28, ndime 2)