Magazini Yophunzira
OCTOBER 2022
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: DECEMBER 5, 2022–JANUARY 1, 2023
© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Ena mwa abale ndi alongo athu olimba mtima omwe anamangidwapo kapena ali m’ndende chifukwa chokhala okhulupirika ku ulamuliro wa Yehova (Onani nkhani yophunzira 42, ndime 1-2)