Magazini Yophunzira
NOVEMBER 2022
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JANUARY 2-29, 2023
© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Ezekieli akuona masomphenya a galeta la Yehova la kumwamba zomwe zikumuthandiza kukhala wotsimikiza kuchita utumiki wake (Onani nkhani yophunzira 45, ndime 7)