Magazini Yophunzira
JANUARY 2023
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: FEBRUARY 27–APRIL 2, 2023
© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
LEMBA LA CHAKA CHA 2023:
“Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha.”—SAL. 119:160
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Akatswiri okopera Malemba a Chiheberi anayesetsa kuchita zimenezo mosamala kwambiri kuti Mawu a Mulungu omwe anakopera akhale olondola (Onani nkhani yophunzira 1, ndime 5)