Magazini Yophunzira
OCTOBER 2023
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: DECEMBER 11, 2023–JANUARY 7, 2024
© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Taganizirani nthawi imene onse kumwamba ndi padziko lapansi adzakhale ogwirizana komanso okhulupirika kwa Yehova. (Onani nkhani yophunzira 44, ndime 8)