Magazini Yophunzira
DECEMBER 2023
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: FEBRUARY 5–MARCH 3, 2024
© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Alongo ndi abale ambiri achinyamata amene anaphunzitsidwa mfundo za m’Malemba n’kumazitsatira amakula mwauzimu (Onani nkhani yophunzira 52 ndime 21, ndi nkhani yophunzira 53, ndime 19-20)