Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • w24.09
  • Magazini Yophunzira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Magazini Yophunzira
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
w24.09
Yesu wakhala pampando kumwamba ndipo akuona magulu awiri a anthu. Zithunzi: Abale ndi alongo akulambira Yehova. 1. Mlongo watenga tabuleti ndipo akuyang’ana kumwamba. 2. Banja likuwerenga Baibulo. 3. Abale ndi alongo akugwira ntchito zomangamanga. 4. M’bale ali kundende ndipo akupemphera. 5. Mlongo wachikulire akuyankha pamisonkhano. 6. Mlongo amene wagonekedwa m’chipatala akupereka kapepala kwa munthu wogwira ntchito m’chipatalamo. 7. Bambo akuphunzira ndi banja lake. Zithunzi: Amuna ndi akazi akuchita zinthu zosemphana ndi mfundo za m’Baibulo. 1. Bambo akupemphera kumalo opangira juga. 2. Mwamuna akumenya mkazi. 3. Anthu okwiya akuchita zionetsero. 4. Bambo wanyamula mfuti ndipo akulondola mayi wina pamalo oimika galimoto. 5. M’busa akupempherera asilikali. 6. Mkazi akugwiritsa ntchito mankhwala osokoneza bongo.

Magazini Yophunzira

SEPTEMBER 2024

NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: NOVEMBER 11–DECEMBER 8, 2024

© 2024 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwakufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.

Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani