Benjamin Boothroyd—Katswiri wa Baibulo Yemwe Anadziphunzitsa Yekha
Ngakhale kuti sanapite kusukulu komanso sanachokere ku banja lolemera, Benjamin anadziphunzitsa yekha Chiheberi, anaphunzira Malemba kenako anamasulira Baibulo la Chingelezi limene lili ndi dzina la Mulungu.