2 SAMUELI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
Davide anakhala mfumu ya Yuda (1-7)
Isi-boseti anakhala mfumu ya Isiraeli (8-11)
Nkhondo ya pakati pa anthu a Davide ndi anthu a Sauli (12-32)
3
Davide anakhala wamphamvu (1)
Ana a Davide (2-5)
Abineri anakhala mbali ya Davide (6-21)
Yowabu anapha Abineri (22-30)
Davide analira maliro a Abineri (31-39)
4
5
Davide anakhala mfumu ya Aisiraeli onse (1-5)
Yerusalemu analandidwa (6-16)
Davide anagonjetsa Afilisiti (17-25)
6
7
Davide anamuletsa kumanga kachisi (1-7)
Pangano la ufumu ndi Davide (8-17)
Pemphero la Davide loyamikira (18-29)
8
9
10
11
Davide anachita chigololo ndi Bati-seba (1-13)
Davide anakonza zoti Uriya aphedwe (14-25)
Davide anakwatira Bati-seba (26, 27)
12
Natani anadzudzula Davide (1-15a)
Mwana wa Bati-seba anamwalira (15b-23)
Bati-seba anabereka Solomo (24, 25)
Mzinda wa Aamoni wa Raba unalandidwa (26-31)
13
Aminoni anagwiririra Tamara (1-22)
Abisalomu anapha Aminoni (23-33)
Abisalomu anathawira ku Gesuri (34-39)
14
Yowabu anatuma mzimayi wa ku Tekowa (1-17)
Davide anatulukira mapulani a Yowabu (18-20)
Abisalomu analoledwa kuti abwerere (21-33)
15
Chiwembu cha Abisalomu (1-12)
Davide anathawa mu Yerusalemu (13-30)
Ahitofeli anagwirizana ndi Abisalomu (31)
Husai anatumidwa kukasokoneza malangizo a Ahitofeli (32-37)
16
Ziba ananamizira Mefiboseti (1-4)
Simeyi ananyoza Davide (5-14)
Abisalomu anamulandira Husai (15-19)
Malangizo a Ahitofeli (20-23)
17
18
19
Davide analira Abisalomu (1-4)
Yowabu anadzudzula Davide (5-8a)
Davide anabwerera ku Yerusalemu (8b-15)
Simeyi anapempha kuti amukhululukire (16-23)
Mefiboseti anasonyeza kuti anali wosalakwa (24-30)
Barizilai analemekezedwa (31-40)
Mkangano pakati pa mafuko (41-43)
20
Sheba anaukira Davide; Yowabu anapha Amasa (1-13)
Anthu anasakasaka Sheba ndipo anadulidwa mutu (14-22)
Ulamuliro wa Davide (23-26)
21
22
23
24
Davide anachimwa powerenga anthu (1-14)
Mliri unapha anthu 70,000 (15-17)
Davide anamanga guwa (18-25)