EZEKIELI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
3
4
5
6
7
Mapeto afika (1-27)
Tsoka loti silinaonekepo (5)
Ndalama zidzatayidwa mʼmisewu (19)
Kachisi adzaipitsidwa (22)
8
9
10
Anatenga moto kuchokera pakati pa mawilo (1-8)
Anafotokoza zokhudza akerubi komanso mawilo (9-17)
Ulemerero wa Yehova unachoka pakachisi (18-22)
11
Anadzudzula akalonga oipa (1-13)
Lonjezo lakubwezeretsa (14-21)
Ulemerero wa Mulungu unachoka mu Yerusalemu (22, 23)
Ezekieli anabwerera ku Kasidi mʼmasomphenya (24, 25)
12
13
14
15
16
17
18
19
20
Mbiri ya kupanduka kwa Isiraeli (1-32)
Aisiraeli analonjezedwa kuti adzabwerera kwawo (33-44)
Ulosi wokhudza mbali yakumʼmwera (45-49)
21
Mulungu adzasolola lupanga lake lachiweruzo (1-17)
Mfumu ya Babulo idzaukira Yerusalemu (18-24)
Mtsogoleri woipa wa Isiraeli adzachotsedwa pa udindo (25-27)
Lupanga lidzapha mbadwa za Amoni (28-32)
22
Yerusalemu, mzinda wa mlandu wokhetsa magazi (1-16)
Isiraeli ali ngati zinthu zachabechabe zotsalira poyenga zitsulo (17-22)
Anadzudzula atsogoleri komanso anthu a mu Isiraeli (23-31)
23
24
25
Ulosi wokhudza Amoni (1-7)
Ulosi wokhudza Mowabu (8-11)
Ulosi wokhudza Edomu (12-14)
Ulosi wokhudza Filisitiya (15-17)
26
27
28
Ulosi wokhudza mfumu ya Turo (1-10)
Nyimbo yoimba polira yokhudza mfumu ya Turo (11-19)
“Iwe unali mu Edeni” (13)
“Kerubi wodzozedwa amene amagwira ntchito yoteteza” (14)
“Unayamba kuchita zinthu zosalungama” (15)
Ulosi wokhudza Sidoni (20-24)
Isiraeli adzabwezeretsedwa mwakale (25, 26)
29
30
31
32
33
Ntchito za mlonda (1-20)
Nkhani yokhudza kuwonongedwa kwa Yerusalemu (21, 22)
Uthenga wopita kwa anthu okhala mʼmabwinja a ku Yerusalemu (23-29)
Anthu atamva uthengawo, sanachite chilichonse (30-33)
34
35
36
37
38
39
Gogi ndi magulu ake a asilikali adzawonongedwa (1-10)
Adzaikidwa mʼmanda mʼChigwa cha Hamoni-Gogi (11-20)
Isiraeli adzabwereranso mwakale (21-29)
40
Ezekieli anamupititsa ku Isiraeli mʼmasomphenya (1, 2)
Ezekieli anaona masomphenya a kachisi (3, 4)
Mabwalo ndi mageti (5-47)
Geti lakunja lakumʼmawa (6-16)
Bwalo lakunja; mageti ena (17-26)
Bwalo lamkati ndi mageti (27-37)
Zipinda zochitiramo utumiki wapakachisi (38-46)
Guwa lansembe (47)
Khonde la kachisi (48, 49)
41
Malo opatulika amʼkachisi (1-4)
Khoma komanso zipinda zamʼmbali (5-11)
Nyumba imene inali kumadzulo (12)
Anayeza nyumba zonse (13-15a)
Mkati mwa kachisi (15b-26)
42
43
44
Geti lakumʼmawa linkakhala lotseka (1-3)
Malangizo okhudza alendo (4-9)
Malangizo okhudza Alevi ndi ansembe (10-31)
45
Chopereka chopatulika komanso mzinda (1-6)
Malo amene mtsogoleri ankalandira (7, 8)
Atsogoleri azichita zinthu moona mtima (9-12)
Zinthu zimene anthu ankapereka komanso zimene mtsogoleri ankayenera kuchita (13-25)
46
Nsembe zoperekedwa pazochitika zapadera (1-15)
Cholowa chochokera pamalo a mtsogoleri (16-18)
Malo amene ankawiritsirapo nsembe (19-24)
47
48