DANIELI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Yerusalemu anazunguliridwa ndi Ababulo (1, 2)
Anyamata amene anatengedwa kupita ku ukapolo analandira maphunziro apadera (3-5)
Chikhulupiriro cha Aheberi 4 chinayesedwa (6-21)
2
Mfumu Nebukadinezara inalota maloto ochititsa mantha (1-4)
Anthu anzeru analephera kumasulira maloto (5-13)
Danieli anapempha Mulungu kuti amuthandize (14-18)
Anatamanda Mulungu chifukwa anawaululira chinsinsi (19-23)
Danieli anauza mfumu maloto ake (24-35)
Kumasulira maloto (36-45)
Danieli analemekezedwa ndi mfumu (46-49)
3
Fano lagolide la Mfumu Nebukadinezara (1-7)
Aheberi atatu anawaneneza kuti sakumvera (8-18)
Anaponyedwa mungʼanjo yamoto (19-23)
Anapulumutsidwa modabwitsa mungʼanjo yamoto (24-27)
Mfumu inalemekeza Mulungu wa Aheberi (28-30)
4
Mfumu Nebukadinezara inavomereza kuti Mulungu ndi woyenera kukhala mfumu (1-3)
Maloto a mfumu okhudza mtengo (4-18)
Danieli anamasulira maloto (19-27)
Kukwaniritsidwa koyamba pa mfumu (28-36)
Mfumu inalemekeza Mulungu wakumwamba (37)
5
Phwando la Mfumu Belisazara (1-4)
Dzanja linalemba pakhoma (5-12)
Danieli anapemphedwa kuti amasulire zimene dzanja linalemba (13-25)
Kumasulira kwake: Babulo adzagwa (26-31)
6
Nduna za Perisiya zinakonzera Danieli chiwembu (1-9)
Danieli anapitiriza kupemphera (10-15)
Danieli anaponyedwa mʼdzenje la mikango (16-24)
Mfumu Dariyo inalemekeza Mulungu wa Danieli (25-28)
7
Masomphenya a zilombo 4 (1-8)
Wamasiku Ambiri anayamba kuweruza mlandu (9-14)
Danieli anauzidwa kumasulira kwake (15-28)
Zilombo 4 zikuimira mafumu 4 (17)
Oyera adzalandira ufumu (18)
Padzakhala nyanga kapena kuti mafumu 10 (24)
8
9
Pemphero la Danieli lolapa machimo (1-19)
Gabirieli anapita kwa Danieli (20-23)
Ananeneratu za milungu 70 yaulosi (24-27)
10
11
12