AFILIPI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Moni (1, 2)
Kuthokoza Mulungu; Pemphero la Paulo (3-11)
Uthenga wabwino unafalikira kwambiri ngakhale kuti panali mavuto (12-20)
Ndikhala ndi moyo kuti ndizitumikira Khristu, ndikamwalira ndipindula (21-26)
Makhalidwe anu azigwirizana ndi uthenga wabwino (27-30)
2
Akhristu azikhala odzichepetsa (1-4)
Kudzichepetsa kwa Khristu komanso kukwezedwa kwake (5-11)
Yesetsani kuti mudzapulumuke (12-18)
Anatumiza Timoteyo ndi Epafurodito (19-30)
3
4
Mgwirizano, kusangalala, maganizo abwino (1-9)
Anayamikira mphatso zimene Afilipi anapereka (10-20)
Moni womaliza (21-23)