Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • g21.3 7
  • Fufuzani Umboni

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Fufuzani Umboni
  • Galamukani!—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Moyo Unayamba Bwanji?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Muzikhulupirira Kwambiri Mlengi
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2021
  • Muzigwiritsa Ntchito Mavidiyo Pophunzira ndi Anthu
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Galamukani!—2021
g21.3 7
Wachinyamata ali mu laibulale ndipo akuwerenga kabuku kakuti “Kodi Zamoyo Zinachita Kulengedwa?” pa tabuleti yake.

Fufuzani Umboni

Magazini ya Galamukani! ino ikufotokoza maumboni ena amene amasonyeza kuti zinthu zam’chilengedwechi zinachita kulengedwa. Fufuzani umboni umenewu ndipo onani ngati pali zifukwa zomveka zimene zingakuchititseni kukhulupirira kuti kuli Mlengi. M’munsimu, muli mitu ya mavidiyo komanso mabuku ena amene angakuthandizeni kupeza mfundo zina zothandiza. Mungapeze mitu imeneyi pa jw.org.

N’chifukwa chiyani anthu ambiri ophunzira amakhulupirira kuti kuli Mlengi?

Onerani zimene ena anafotokoza pa mavidiyo akuti “Zokhudza Mmene Moyo Unayambira.”

Kodi pali mfundo zomveka zotsimikizira kuti zamoyo zinachita kusintha?

Werengani kabuku kakuti Kodi Zamoyo Zinachita Kulengedwa?

Kodi n’zomveka kukhulupirira kuti kuli Mlengi?

Onerani vidiyo yakuti Zimene Achinyamata Anzanu Amanena—Kukhulupirira Kuti Kuli Mulungu.

Kodi ndi nzeru kukhulupirira Baibulo?

Werengani kabuku kakuti Mmene Moyo Unayambira—Mafunso 5 Ofunika Kwambiri.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani