Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • lfb sect. 1
  • Mawu Oyamba Gawo 1

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu Oyamba Gawo 1
  • Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Nkhani Yofanana
  • Muziphunzira Zambiri Zokhudza Yehova Poona Chilengedwe Chake
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Muzigwiritsa Ntchito Chilengedwe Pophunzitsa Ana Anu Zokhudza Yehova
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Mmene Chilengedwe Chimasonyezera Kuti Mulungu Ndi Wachikondi
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Mulungu Analenga Kumwamba ndi Dziko Lapansi
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Onani Zambiri
Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
lfb sect. 1
Anthu akusangalala ndi chilengedwe

Mawu Oyamba Gawo 1

Baibulo limayamba n’kufotokoza zokhudza chilengedwe ndipo izi zimatithandiza kuyamikira zinthu zokongola zimene Yehova analenga zakumwamba komanso zapadzikoli. Ngati ndinu kholo, thandizani mwana wanu kuti athe kuzindikira mfundo yoti Mulungu analenga zinthu zodabwitsa zosiyanasiyana. Fotokozani kuti Mulungu anatilenga anthufe mwapamwamba kusiyana ndi zinyama. Anatilenga m’njira yakuti tizitha kulankhula, kuganiza, kupanga zinthu, kuimba komanso kupemphera. Muthandizeninso kudziwa kuti Yehova ali ndi mphamvu, nzeru komanso chikondi. Ndipo amakonda zolengedwa zake kuphatikizapo ifeyo, aliyense payekha.

ZIMENE TIPHUNZIRE M’CHIGAWOCHI

  • Yehova ndi Mwana wake analenga dzikoli kuti tizikhalamo

  • Yehova anayambitsa banja pamene analenga mwamuna ndi mkazi n’kuwapatsa mwayi woti azibereka ana

  • Cholinga cha Yehova n’choti anthu adzakhale ndi moyo wosatha, mwamtendere komanso mogwirizana

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani