Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • lfb sect. 6
  • Mawu Oyamba Gawo 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu Oyamba Gawo 6
  • Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Nkhani Yofanana
  • Aisiraeli Analowa M’dziko la Kanani
    Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?
  • “Kumene Inu Mupite Inenso Ndipita Komweko”
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Zimene Yefita Analonjeza
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Rute ndi Naomi
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Onani Zambiri
Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
lfb sect. 6
Samisoni wanyamula geti la mzinda wa Gaza

Mawu Oyamba Gawo 6

Aisiraeli atafika m’Dziko Lolonjezedwa ankalambira Mulungu kuchihema. Ansembe ankaphunzitsa Chilamulo ndipo oweruza ndi amene ankatsogolera anthu. Chigawochi chikufotokoza mmene zosankha komanso zochita za munthu zimakhudzira anthu ena. Mwisiraeli aliyense ankafunikira kukonda Yehova komanso anthu ena. Fotokozani mmene zochita za Debora, Naomi, Yoswa, Hana, mwana wamkazi wa Yefita komanso Samueli zinathandizira anthu ena. Tsindikani mfundo yakuti ngakhale anthu a mitundu ina anasankha kugwirizana ndi Aisiraeli chifukwa ankadziwa kuti Mulungu ankawatsogolera. Chitsanzo pa nkhaniyi ndi Rahabi, Rute, Yaeli ndiponso anthu a ku Gibiyoni.

ZIMENE TIPHUNZIRE M’CHIGAWOCHI

  • Yehova anagwiritsa ntchito oweruza populumutsa anthu ake modabwitsa

  • Yehova anadalitsa anthu onse okhulupirika omwe ankamudalira

  • Mulungu alibe tsankho, amalandira anthu ochokera mu mtundu uliwonse omwe amamukonda ndi kuchita zabwino

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani