Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • lfb sect. 10
  • Mawu Oyamba Gawo 10

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu Oyamba Gawo 10
  • Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Nkhani Yofanana
  • Anakana Kulambira Fano
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Analimba Mtima Kuteteza Anthu a Mulungu
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Anachita Zinthu Mwanzeru, Molimba Mtima Ndiponso Moganizira Ena
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Danieli Anaponyedwa M’dzenje la Mikango
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
lfb sect. 10
Mfumu Ahasiwero waloza Mfumukazi Esitere ndi ndodo yake

Mawu Oyamba Gawo 10

Yehova ndi Mfumu ya chilengedwe chonse. Iye wakhala akulamulira kuyambira kalekale ndipo sadzasiya. Mwachitsanzo, iye anapulumutsa Yeremiya ataponyedwa m’chitsime kuti afe. Anapulumutsanso Shadireki, Misheki ndi Abedinego m’ng’anjo ya moto ndiponso anapulumutsa Danieli m’dzenje la mikango. Iye anatetezanso Esitere n’cholinga choti apulumutse anthu a mtundu wake. Yehova sadzalola kuti zoipa zizingopitirizabe. Ulosi wonena za chifaniziro chachikulu komanso mtengo waukulu umasonyeza kuti Ufumu wa Yehova udzathetsa mavuto onse ndipo udzalamulira dziko lonse.

ZIMENE TIPHUNZIRE M’CHIGAWOCHI

  • Ufumu wa Yehova ndi wamphamvu kuposa boma lililonse la anthu

  • Tiyenera kukhala olimba mtima ngati Esitere ndi Danieli n’kumachita zoyenera kulikonse komwe tili

  • Tikapanikizika ndi mavuto tizidalira kwambiri Yehova ngati mmene anachitira Yeremiya ndi Nehemiya

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani