Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • lff sect. 3
  • Mavidiyo ndi Zinthu Zina za Gawo 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mavidiyo ndi Zinthu Zina za Gawo 3
  • Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Nkhani Yofanana
  • Mavidiyo ndi Zinthu Zina za mu Gawo 2
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Mavidiyo ndi Zinthu Zina za mu Gawo 4
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Mavidiyo ndi Zinthu Zina za mu Gawo 1
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Mavidiyo ndi Zinthu Zina
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Yambani Kuphunzira Baibulo
Onani Zambiri
Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
lff sect. 3

Mavidiyo ndi Zinthu Zina za Gawo 3

  1. 34 Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timakonda Yehova?

  2. 35 N’chiyani Chingatithandize Kuti Tizisankha Zinthu Mwanzeru?

  3. 36 Muzichita Zinthu Zonse Moona Mtima

  4. 37 Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani ya Ntchito Komanso Ndalama

  5. 38 Muziona Kuti Moyo Ndi Mphatso Yamtengo Wapatali

  6. 39 Mmene Mulungu Amaonera Magazi

  7. 40 Tingatani Kuti Mulungu Azitiona Kuti Ndife Oyera?

  8. 41 Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Kugonana?

  9. 42 Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yokhala Pabanja Ndi Kusakhala Pabanja?

  10. 43 Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Mowa?

  11. 44 Kodi Zikondwerero Zonse Zimasangalatsa Mulungu?

  12. 45 Kodi Kusakhala Mbali ya Dziko Kumatanthauza Chiyani?

  13. 46 N’chifukwa Chiyani Muyenera Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa?

  14. 47 Kodi Mwakonzeka Kubatizidwa?

34 Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timakonda Yehova?

Muzilalikira Molimba Mtima Ngakhale Mukutsutsidwa (5:09)

ONANI ZINANSO

“Munthu Wokhulupirika, Mudzamuchitira Mokhulupirika” (16:49)

“Yobu Anapitiriza Kutumikira Mulungu ndi Mtima Wosagawanika” (Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani? gawo 6)

Uzisangalatsa Yehova (8:16)

Musamangotengera Zochita za Anzanu (3:59)

35 N’chiyani Chingatithandize Kuti Tizisankha Zinthu Mwanzeru?

Muzitsatira Mfundo za M’Baibulo Mukamasankha Zochita (5:54)

“Khalani ndi Chikumbumtima Chabwino” (5:13)

ONANI ZINANSO

“Zosankha Zanu Zizilemekeza Mulungu” (Nsanja ya Olonda, April 15, 2011)

Yehova Amatsogolera Anthu Ake (9:50)

Yehova Amatipatsa Zinthu Zabwino Zokhazokha (5:46)

“Kodi Mumafunikira Lamulo la M’Baibulo Nthawi Zonse?” (Nsanja ya Olonda, December 1, 2003)

36 Muzichita Zinthu Zonse Moona Mtima

Zimene Zimatithandiza Kukhala Osangalala​​—Chikumbumtima Chabwino (2:32)

ONANI ZINANSO

Uzinena Zoona (1:44)

Anthu Omwe Amachita Zimene Alonjeza Amadalitsidwa (9:09)

“Kodi Muyenera Kukhoma Misonkho?” (Nsanja ya Olonda, September 1, 2011)

“Ndinaphunzira Kuti Yehova Ndi Wachifundo Komanso Amakhululuka” (Nsanja ya Olonda, May 1, 2015)

37 Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani ya Ntchito Komanso Ndalama

Muzigwira Ntchito Ndi Moyo Wonse Ngati Kuti Mukugwirira Yehova (4:39)

‘Muzikhala Okhutira Ndi Zimene Muli Nazo’ (3:20)

Yehova Adzatisamalira (6:21)

ONANI ZINANSO

“Kodi Ndalama ndi Zimene Zimabweretsa Mavuto Onse?” (Nkhani yapawebusaiti)

“Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Kupatsa?” (Nkhani yapawebusaiti)

“Zimene Baibulo Limanena​—Kutchova Juga” (Galamukani!, March 2015)

“Baibulo Limasintha Anthu” (Nsanja ya Olonda, November 1, 2011)

38 Muziona Kuti Moyo Ndi Mphatso Yamtengo Wapatali

Muziyesetsa Kupewa Ngozi (8:34)

Muziona Moyo Mmene Yehova Amauonera (5:00)

ONANI ZINANSO

Nyimbo 141​—Moyo Ndi Wodabwitsa (2:41)

“Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yochotsa Mimba?” (Nkhani yapawebusaiti)

“‘Masewera Angozi’​—Kodi Muyenera Kuika Moyo Wanu Pachiswe Mwakuwachita?” (Galamukani!, October 8, 2000)

“Kodi Baibulo Lingandithandize Ngati Ndili ndi Maganizo Ofuna Kudzipha?” (Nkhani yapawebusaiti)

39 Mmene Mulungu Amaonera Magazi

Mungasankhe Bwanji Zoyenera Kuchita pa Nkhani ya Thandizo Lachipatala Lokhudza Magazi? (5:47)

Zimene Ananena Pulofesa Massimo P. Franchi, M.D. (1:36)

ONANI ZINANSO

“Mafunso Ochokera kwa Owerenga” (Nsanja ya Olonda, October 15, 2000)

“Mafunso Ochokera kwa Owerenga” (Nsanja ya Olonda, June 15, 2004)

“Ndinayamba Kuona Magazi Mmene Mulungu Amawaonera” (Galamukani!, December 8, 2003)

Yehova Amathandiza Anthu Amene Akudwala (10:23)

40 Tingatani Kuti Mulungu Azitiona Kuti Ndife Oyera?

Mulungu Amakonda Anthu Aukhondo (4:10)

Mudzikhala Odziletsa (2:47)

Yesetsani Kuti Mukhale Oyera (1:51)

“Kodi Ndingatani Kuti Ndisiye Chizolowezi Choseweretsa Maliseche?” (Mayankho a Zimene Achinyamata Amadzifunsa, Buku Loyamba, mutu 25)

ONANI ZINANSO

Moyo Wathanzi Komanso Ukhondo​—Kusamba M’manja (3:01)

“N’zotheka Kusiya Fodya” (Galamukani!, May 2010)

“Kodi Kuonera Zolaula Kuli Ndi Mavuto Otani?” (Nsanja ya Olonda, August 1, 2013)

“Ndinasintha Khalidwe Langa Movutikira Kwambiri” (Nsanja ya Olonda Na. 4 2016)

41 Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Kugonana?

Thawani Dama (5:06)

Muziwerenga Baibulo Kuti Musagonje pa Mayesero (3:02)

Wopanda Nzeru Mumtima (9:31)

ONANI ZINANSO

“Kodi Baibulo Limavomereza Kuti Mwamuna ndi Mkazi Azikhalira Limodzi Asanakwatirane?” (Nkhani yapawebusaiti)

“Kodi Kugonana Kwa Amuna Kapena Akazi Okhaokha N’kolakwika?” (Nkhani yapawebusaiti)

“Kodi Kugonana M’kamwa Kumakhaladi Kugonana?” (Nkhani yapawebusaiti)

“Baibulo Limasintha Anthu” (Nsanja ya Olonda, April 1, 2011)

42 Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yokhala Pabanja Ndi Kusakhala Pabanja?

Akhristu Okhulupirika Omwe Sali Pabanja (3:11)

Banja Ndi Mgwirizano Wamoyo Wonse (4:30)

N’zotheka Kutsatira Mfundo za Yehova Zokhudza Ukwati (4:14)

ONANI ZINANSO

“Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga” (Nsanja ya Olonda, July 1, 2004)

Kukonzekera Banja (17:05)

Ndinkakhulupirira Kuti Nayenso Akhoza Kuphunzira Choonadi (1:56)

“Tizilemekeza ‘Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi’” (Nsanja ya Olonda, December 2018)

43 Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Mowa?

Kodi Padzakhale Mowa Kapena Ayi? (2:41)

‘Khalidwe Langa Loipa Linanditopetsa’ (6:32)

ONANI ZINANSO

Ganizirani Zimene Zingachitike Ngati Mutamwa Mowa (2:31)

“Khalani ndi Maganizo Oyenera Pankhani ya Kumwa Mowa” (Nsanja ya Olonda, January 1, 2010)

“Mafunso Ochokera kwa Owerenga” (Nsanja ya Olonda, February 15, 2007)

“Baibulo Limasintha Anthu” (Nsanja ya Olonda, May 1, 2012)

44 Kodi Zikondwerero Zonse Zimasangalatsa Mulungu?

Maholide Komanso Zikondwerero Zimene Mulungu Sasangalala Nazo (5:07)

Muzifotokoza Zimene Mumakhulupirira Mosamala (2:01)

Kulandira Alendo pa Misonkhano ya Mayiko (5:40)

ONANI ZINANSO

“N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sachita Nawo Maholide Ena?” (Nkhani yapawebusaiti)

“N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sakondwerera Masiku Akubadwa?” (Nkhani yapawebusaiti)

Muzichita Zinthu Mosamala Ena Akamakunyozani (2:04)

“Amasangalala Ngakhale Kuti Sachita Khirisimasi” (Nsanja ya Olonda, December 1, 2012)

45 Kodi Kusakhala Mbali ya Dziko Kumatanthauza Chiyani?

Akhristu Oona Sakhala Mbali ya Dziko​—Gawo 1 (4:28)

Akhristu Oona Sakhala Mbali ya Dziko​—Gawo 2 (3:11)

Akhristu Oona Sakhala Mbali ya Dziko​—Gawo 3 (1:18)

N’chifukwa Chiyani Akhristu Oona Amafunika Kulimba Mtima Kuti Asalowerere Ndale? (2:49)

Zimene Ndinaphunzira mu Nsanja ya Olonda​—Kusakhala Mbali ya Dzikoli (5:16)

ONANI ZINANSO

Yehova Sanatisiye (3:14)

Tisamachite Zinthu Zosonyeza Kuti Tili Mbali ya Dziko Tikakhala Pagulu (4:25)

“Zinthu Zonse N’zotheka ndi Mulungu” (5:19)

“Yense Adzasenza Katundu Wake wa Iye Mwini” (Nsanja ya Olonda, March 15, 2006)

46 N’chifukwa Chiyani Muyenera Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa?

Kupereka Mphatso Kwa Mulungu (3:04)

Ndinkaona Kuti Kusewera Mpira Kungandithandize Kukhala Wosangalala (5:45)

ONANI ZINANSO

Zimene Achinyamata Amafunsa​—Kodi Ndidzachita Zotani Pamoyo Wanga?​​—Zimene Anasankha (6:54)

“N’chifukwa Chiyani Muyenera Kudzipereka kwa Yehova?” (Nsanja ya Olonda, January 15, 2010)

Ndadzipereka Kwa Inu (4:30)

“Baibulo Limasintha Anthu” (Nsanja ya Olonda, November 1, 2012)

47 Kodi Mwakonzeka Kubatizidwa?

Zimene Munthu Angachite Kuti Abatizidwe (3:56)

Anathana Ndi Zinthu Zomwe Zikanamulepheretsa Kubatizidwa (5:22)

Yehova Mulungu Adzakuthandizani (2:50)

ONANI ZINANSO

“Kodi Ndinu Okonzeka Kubatizidwa?” (Nsanja ya Olonda, March 2020)

“Chikundiletsa Kubatizidwa N’chiyani?” (Nsanja ya Olonda, March 2019)

‘N’chifukwa Chiyani Mukuzengereza Kubatizidwa?’ (1:10)

Ndine Woyenereradi Kulandira Madalitso Onsewa? (7:21)

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani