Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • CA-brpgm22 3
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  • Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2021-2022
  • Nkhani Yofanana
  • Pezani Mayankho a Mafunso Awa
    Msonkhano Wadera wa Mboni za Yehova Wokhala ndi Woyang’anira Dera wa 2021-2022
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
    Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2023-2024
  • Limbitsani Chikhulupiriro Chanu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2021-2022
  • Muzisonyeza Kuti Mumakhulupirira Malonjezo a Yehova
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
Onani Zambiri
Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2021-2022
CA-brpgm22 3

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa:

  1. 1. N’chifukwa chiyani tiyenera kulimbitsa chikhulupiriro chathu panopa? (Aheb. 10:39)

  2. 2. Kodi “tingaone” bwanji Yehova ngakhale kuti iye ndi wosaoneka? (Aheb. 11:27)

  3. 3. N’chifukwa chiyani n’zofunika kuti tiziphunzira maulosi a m’Baibulo? (Aroma 10:17)

  4. 4. Kodi mzimu woyera ungatithandize bwanji kuti tikhale ndi chikhulupiriro? (Luka 11:13; Agal. 5:22)

  5. 5. Kodi tingathandize bwanji ena kukhala ndi chikhulupiriro cholimba? (1 Ates. 2:7, 8)

  6. 6. N’chifukwa chiyani tiyenera kuyang’anitsitsa “Mtumiki Wamkulu ndi Wokwaniritsa chikhulupiriro chathu”? (Aheb. 12:2, 3)

© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

CA-brpgm22-CN

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani