NYIMBO 160
“Uthenga Wabwino”
zosindikizidwa
1. Tilemekeze M’lungu
Amatikonda.
Anatumiza Mwana wake
Kudzatipatsa
Chiyembekezochi.
(KOLASI)
Uthengawu ndi
Wosangalatsa.
Ndi wabwinodi.
Tilalikire
Za uthengawu.
Khristu wabadwa,
Mpulumutsi wathu.
2. Azidzalamulira
Mwachilungamo.
Abweretsa Paradaiso
Ndipo Ufumu
Wakewo sudzatha.
(KOLASI
Uthengawu ndi
Wosangalatsa.
Ndi wabwinodi.
Tilalikire
Za uthengawu.
Khristu wabadwa,
Mpulumutsi wathu.
(KOLASI)
Uthengawu ndi
Wosangalatsa.
Ndi wabwinodi.
Tilalikire
Za uthengawu.
Khristu wabadwa,
Mpulumutsi wathu.
(Onaninso Mat. 24:14; Yoh. 8:12; 14:6; Yes. 32:1; 61:2.)