‘Sitichita Manyazi ndi Uthenga Wabwino’
M’mawa
9:40 Kumvetsera Nyimbo
9:50 Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero
10:00 N’chifukwa Chiyani ‘Sitichita Manyazi ndi Uthenga Wabwino’?
10:15 Muzilalikira Molimba Mtima Uthenga Wabwino
10:30 Mukhale “Munthu Wosachita Manyazi ndi Ntchito Imene Wagwira”
10:55 Nyimbo Na. 73 ndi Zilengezo
11:05 Muzisonyeza Kuti Ndinu Wamphamvu, Wachikondi Komanso Woganiza Bwino
11:35 Nkhani ya Ubatizo: Pitirizani ‘Kugonjera Uthenga Wabwino’
12:05 Nyimbo Na. 75
Masana
1:20 Kumvetsera Nyimbo
1:30 Nyimbo Na. 77
1:35 Zochitika pa Moyo wa Chikhristu
1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:15 Nkhani Yosiyirana: Sitichita Manyazi . . .
• Ndi Mfundo za Mulungu za Makhalidwe Abwino
• Ndi Ufumu wa Mulungu
• Ndi Anthu Amene Akutsogolera M’gulu la Mulungu
3:00 Nyimbo Na. 40 ndi Zilengezo
3:10 ‘Muzidzitama mwa Yehova’
3:55 Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero