Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.01 1
  • Zitsanzo za Ulaliki

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zitsanzo za Ulaliki
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • ●○○ULENDO WOYAMBA
  • ○●○ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA
  • ○○●ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI
  • Mmene Tingagwiritsire Ntchito Zitsanzo za Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Mmene Tingagwiritsire Ntchito Zitsanzo za Zimene Tinganene
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.01 1
Akugawira kapepala kufupi ndi mzinda wa Monrovia ku Liberia

Akugawira kapepala kufupi ndi mzinda wa Monrovia ku Liberia

Zimene Tinganene

●○○ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi inuyo mumaona kuti Baibulo ndi lothandizabe masiku ano?

Lemba: 2 Tim. 3:16

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi m’Baibulo muli uthenga wotani?

○●○ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA

Funso: Kodi m’Baibulo muli uthenga wotani?

Lemba: Mat. 6:10

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Ufumu wa Mulungu udzachita chiyani?

○○●ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI

Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu udzachita chiyani?

Lemba: Dan. 2:44

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi zimenezi zidzakhudza bwanji anthu omwe ali padzikoli?

Poyamba, Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu inkakhala ndi zitsanzo za ulaliki zitatu zokhala ndi nkhani zosiyana. Koma kuyambira ndi mwezi uno, tizikhala ndi zitsanzo za zimene tinganene ndipo zizikhala ndi funso, lemba komanso funso lodzakambirana pa ulendo wotsatira. Zitsanzo ziwiri zizikhala za ulendo wobwereza woyamba ndi wachiwiri. Mlungu uliwonse pazikhala vidiyo imodzi yosonyeza zimene tinganene. Panopa wofalitsa azisankha yekha buku kapena zinthu zina zimene akufuna kugwiritsa ntchito pa ulendo woyamba kapena pa ulendo wobwereza. Buku kapena zinthu zimenezi zizikhala zimene tinauzidwa kuti tizigwiritsa ntchito mu utumiki. Zimenezi zitithandiza kukwaniritsa cholinga chathu chomwe ndi kuphunzitsa ‘onse amene ali ndi maganizo abwino amene angawathandize kukapeza moyo wosatha.’​—Mac.13:48.

Nkhani za Ophunzira: Ophunzira ayenera kugwiritsa ntchito zitsanzo za zimene tinganene kupatulapo ngati apatsidwa malangizo ena.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani