Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.01 4
  • Pitirizani Kufunafuna Ufumu Choyamba

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Pitirizani Kufunafuna Ufumu Choyamba
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Nsembe Yosonyeza Kuyamikira
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • 4 Kodi Tiyenera Kupemphera za Chiyani?
    Nsanja ya Olonda—2010
  • Mukhale ndi Zolinga mu Chaka Chautumiki Chikubwerachi​—Thandizani pa Ntchito Yazomangamanga
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.01 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 6-7

Pitirizani Kufunafuna Ufumu Choyamba

M’pemphero lachitsanzo, Yesu anasonyeza kuti zinthu zokhudza kukwaniritsidwa kwa cholinga cha Yehova komanso Ufumu wa Mulungu ndi zimene ziyenera kukhala zofunika kwambiri pamoyo wathu.

6:9-13

  • Yesu ali kumwamba pampando wake wachifumu

    Dzina la Mulungu

    Ufumu wa Mulungu

    Chifuniro cha Mulungu

  • Mkate

    Chakudya cha tsiku ndi tsiku

    Kukhululukidwa machimo

    Kupulumutsidwa pa mayesero

Zinthu zina zokhudza Ufumu zimene ndiyenera kupempherera:

  • Ntchito yolalikira ipite patsogolo

  • Mzimu woyera uthandize anthu amene akuzunzidwa

  • Mulungu adalitse ntchito yomanga kapena ntchito yolalikira imene yakonzedwa mwapadera

  • Mulungu azipereka nzeru komanso mphamvu kwa anthu amene akutsogolera m’gulu lake

  • Zina

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani