Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.01 6
  • Yesu Ankakonda Anthu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yesu Ankakonda Anthu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.01 6
Yesu akuchiritsa munthu wakhate

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 8-9

Yesu Ankakonda Anthu

Pa Mateyu 8 ndi 9 amafotokoza zokhudza utumiki wa Yesu ku Galileya. Pamene Yesu ankachiritsa anthu, anasonyeza kuti anali ndi mphamvu, koma chofunika kwambiri n’chakuti anasonyezanso kuti amakonda kwambiri anthu ndiponso kuti ndi wachifundo.

  1. Mizinda ya ku Galileya kumene Yesu anachiritsa anthu

    Yesu anachiritsa munthu wakhate.​—Mat. 8:1-3

  2. Yesu anachiritsa wantchito wa mkulu wa asilikali.​—Mat. 8:5-13

    Anachiritsa apongozi aakazi a Petulo.​—Mat. 8:14, 15

    Anatulutsa ziwanda ndiponso anachiritsa odwala.​—Mat. 8:16, 17

  3. Yesu anatulutsa ziwanda mwa amuna awiri ochititsa mantha ndipo anazitumiza kuti zikalowe m’gulu la nkhumba.​—Mat. 8:28-32

  4. Yesu anachiritsa munthu wakufa ziwalo.​—Mat. 9:1-8

    Anachiritsa mayi wina amene anagwira chovala chake ndiponso anaukitsa mwana wa Yairo.​—Mat. 9:18-26

    Anachiritsa munthu wosalankhula komanso akhungu.—Mat. 9:27-34

  5. Yesu ankayenda m’mizinda ndi m’midzi kuchiritsa matenda amtundu uliwonse ndi zofooka zilizonse.​—Mat. 9:35, 36

Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimakonda anthu ena?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani