Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.01 7
  • Yesu Ankatsitsimula Ena

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yesu Ankatsitsimula Ena
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • “Bwerani kwa Ine . . . Ndipo Ndidzakutsitsimutsani”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.01 7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 10-11

Yesu Ankatsitsimula Ena

11:28-30

Mzimayi wa m’nthawi yakale atanyamula goli

“Goli langa ndi lofewa”

Popeza Yesu anali kalipentala, ankadziwa kupanga goli labwino ndipo mwina ankaika nsalu kapena chikopa kuti likhale lofewa. Pamene tinabatizidwa, tinasenza goli la Yesu ndipo tinakhala ophunzira ake. Pa nthawiyi tinasenza udindo waukulu komanso tinayamba kugwira ntchito yolalikira yomwe si yophweka. Komabe timasangalala kuchita zimenezi ndipo timapeza madalitso ambiri.

Kodi mwapeza madalitso otani kuyambira pamene munasenza goli la Yesu?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani