CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 1
Muzitsanzira Mariya Pokhala Odzichepetsa
Yehova anasankha Mariya n’kumupatsa ntchito yapadera chifukwa anali ndi mtima wabwino.
Kodi zimene Mariya analankhula zimasonyeza bwanji kuti . . .
anali wodzichepetsa?
anali ndi chikhulupiriro cholimba?
ankadziwa bwino Malemba?
anali ndi mtima woyamikira?