Ku Myanmar, Akhristu akucheza
Zimene Tinganene
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi n’zoona kuti tili m’masiku otsiriza?
Lemba: 2 Tim. 3:1-5
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi chidzachitike n’chiyani masiku otsiriza akadzatha?
○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA
Funso: Kodi chidzachitike n’chiyani masiku otsiriza akadzatha?
Lemba: Chiv. 21:3, 4
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tingatani kuti tidzapeze madalitso amene Mulungu anatilonjeza?
○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI
Funso: Kodi tingatani kuti tidzapeze madalitso amene Mulungu anatilonjeza?
Lemba: Yoh. 3:16
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi chikhulupiriro chimatanthauza chiyani?