CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 TIMOTEYO 4-6
Kukhala Wodzipereka kwa Mulungu N’kofunika Kuposa Chuma
Kodi malemba otsatirawa akusonyeza bwanji kuti tingakhale osangalala kwambiri ngati titakhala wodzipereka kwa Mulungu m’malo mofunafuna chuma?
Anthu amene akufuna kuyamba utumiki wa nthawi zonse adzapeza madalitso ambiri
N’chifukwa chiyani n’zosatheka kukhala wodzipereka kwa Mulungu pa nthawi imodzimodziyo n’kumafunafuna chuma? (Mat. 6:24)