Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb20.03
  • Zimene Tinganene

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Tinganene
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • ●○○ ULENDO WOYAMBA
  • ○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA
  • ○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI
  • NTCHITO YOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO (14 March–7 April):
  • Zimene Tinganene
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Zimene Tinganene
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20.03
Abulahamu ndi Isaki akupita ku Moriya

Abulahamu anali womvera ndipo anapita ndi Isaki ku Moriya

Zimene Tinganene

●○○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi Yesu ndi ndani?

Lemba: Mt 16:16

Funso la Ulendo Wotsatira: N’chifukwa chiyani Yesu anafa?

LEMBALI LIKUPEZEKA MU:

  • Buku la ‘Zimene Baibulo Limaphunzitsa.’

    bhs 41 ¶5

○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA

Funso: N’chifukwa chiyani Yesu anafa?

Lemba: Mt 20:28

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira nsembe imene Yesu anapereka?

LEMBALI LIKUPEZEKA MU:

  • Buku la ‘Zimene Baibulo Limaphunzitsa.’

    bhs 52 ¶2

○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI

Funso: Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira nsembe imene Yesu anapereka?

Lemba: Yoh 17:3

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi pamisonkhano ya Mboni za Yehova pamachitika zotani?

LEMBALI LIKUPEZEKA MU:

  • Buku la ‘Zimene Baibulo Limaphunzitsa.’

    bhs 58 ¶19

NTCHITO YOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO (14 March–7 April):

“Tikukuitanirani ku mwambo wofunika kwambiri womwe udzachitike padziko lonse. Mwambo umenewu ndi wokumbukira imfa ya Yesu.” Kenako m’patseni kapepala. “Kapepalaka kakusonyeza nthawi komanso malo omwe mwambowu udzachitikire m’dera lathu lino. Tikukuitananinso kuti mudzamvetsere nkhani yapadera yomwe idzakambidwe kutatsala mlungu umodzi kuti mwambowu uchitike.”

Funso la Ulendo Wotsatira Ngati Munthuyo Wasonyeza Chidwi: N’chifukwa chiyani Yesu anafa?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani