CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 24
Isaki Anapeza Mkazi
Mtumiki wa Abulahamu anapempha Yehova kuti amuthandize kusankha mkazi wa Isaki. (Ge 24:42-44) Nafenso tizipempha Yehova kuti atithandize kusankha zoyenera kuchita pa nkhani zikuluzikulu. Kodi tingachite bwanji zimenezi?
Tizipemphera
Tiziwerenga Mawu a Mulungu komanso tizifufuza m’mabuku athu
Tizipempha abale ndi alongo olimba mwauzimu kuti atithandize nzeru