Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb20.03
  • Esau Anagulitsa Ukulu Wake

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Esau Anagulitsa Ukulu Wake
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Yakobo Analandira Madalitso
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Anthu Okonda Yehova Amasankha Zinthu Mwanzeru
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20.03
M’bale akusinkhasinkha zimene wawerenga m’Baibulo. Akuganizira kuti akuona Esau akugulitsa ukulu wake kwa Yakobo pousinthanitsa ndi mbale ya mphodza.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 25-26

Esau Anagulitsa Ukulu Wake

25:27-34

Esau ‘sanayamikire zinthu zopatulika.’ (Ahe 12:16) Iye anagulitsa ukulu wake ndipo kenako anakwatira akazi awiri achikunja.​—Ge 26:34, 35.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimayamikira zinthu zopatulika zotsatirazi?’

  • Ubwenzi wanga ndi Yehova

  • Mzimu woyera

  • Kudziwika ndi dzina loyera la Yehova

  • Ntchito yolalikira

  • Misonkhano

  • Ukwati

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani