Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb20.09 2
  • Musamatsatire Khamu la Anthu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Musamatsatire Khamu la Anthu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Khamu Lalikulu la Anthu Likudalitsidwa ndi Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Muzikhala Okonzeka Kukhululuka
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • “Ndinaona Khamu Lalikulu la Anthu”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20.09 2
Anthu akuonera nyuzi pa mafoni awo komanso pa TV yaikulu m’malo opezeka anthu ambiri.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 23-24

Musamatsatire Khamu la Anthu

23:1-3

Yehova anachenjeza mboni komanso oweruza milandu kuti asamatengeke ndi khamu la anthu kuti apereke umboni wonama kapena kuweruza mopanda chilungamo. Mfundo imeneyi ingatithandizenso pochita zinthu zambiri. Tikutero chifukwa chakuti nthawi zonse Akhristu akufunika kuyesetsa kuti asatengere maganizo komanso makhalidwe oipa am’dzikoli.​—Aro 12:2.

N’chifukwa chiyani si nzeru kutsatira khamu la anthu pamene

  • tamva nkhani zopanda umboni kapena miseche?

  • tikusankha zovala, masitayilo a tsitsi kapena zosangalatsa?

  • tikuganizira kapena kuchita zinthu ndi anthu amtundu wina, chikhalidwe china kapena amene timasiyana nawo pa nkhani ya chuma?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani