Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb20.12 1
  • Zimene Tinganene

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Tinganene
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • ●○ ULENDO WOYAMBA
  • ○● ULENDO WOBWEREZA
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20.12 1
Ansembe ali m’bwalo la chihema chopatulika ndipo akugwira ntchito zawo pafupi ndi beseni la mkuwa komanso guwa la nsembe zopsereza. Wansembe ali m’Malo Oyera patebulo la mkate wachionetsero.

Ansembe akugwira ntchito zawo pachihema

Zimene Tinganene

●○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi tingapeze kuti malangizo otithandiza kukhala ndi moyo wosangalala?

Lemba: Sl 1:1, 2

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi kukonda ndalama komanso chuma kungathandize munthu kuti akhale ndi moyo wosangalala?

LEMBALI LIKUPEZEKA MU:

  • Kabuku ka ‘Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu’

    fg phunziro 12 ¶6

○● ULENDO WOBWEREZA

Funso: Kodi kukonda ndalama komanso chuma kungathandize munthu kuti akhale ndi moyo wosangalala?

Lemba: 1Ti 6:9, 10

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi kuona zinthu moyenera n’kothandiza bwanji?

LEMBALI LIKUPEZEKA MU:

  • Kabuku ka ‘Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu’

    fg phunziro 11 ¶7

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani