Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb22.03 17
  • Tiziyembekezera Yehova Moleza Mtima

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tiziyembekezera Yehova Moleza Mtima
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Tizidzichepetsa Zinthu Zikatiyendera
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Mmene Davide Ankamenyera Nkhondo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani ya Kulimba Mtima Komanso Yochititsa Chidwi
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22.03 17
Davide ndi mmodzi mwa amuna amene anali nawo abisala m’phanga pamene Mfumu Sauli akutulukamo. Davide akuuza mwamunayo, yemwe ali ndi lupanga, kuti asaphe Sauli.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tiziyembekezera Yehova Moleza Mtima

Davide anali ndi mwayi woti akanathetsa mavuto ake (1Sa 24:3-5)

Davide ankaona zimene zinkamuchitikira mmene Yehova ankazionera ndipo anasonyeza kudzichepetsa (1Sa 24:6, 7)

Davide anali ndi chikhulupiriro kuti Yehova adzathetsa mavuto ake (1Sa 24:12, 15; w04 4/1 16 ¶8)

Mofanana ndi Davide, tiyenera kumayembekezera Yehova m’malo mogwiritsa ntchito nzeru zathu pothetsa mavuto amene tikukumana nawo.​—Yak 1:4; w04 6/1 22-23.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani