Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.03 12
  • “Uteteze Mtima Wako”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Uteteze Mtima Wako”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Muziwerenga Baibulo Tsiku Lililonse Komanso Muzifunafuna Nzeru
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Zimene Inuyo Mwachita
    Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso
  • Zimene Tikuphunzira pa Mawu Omaliza a Amuna Okhulupirika
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.03 12

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

“Uteteze Mtima Wako”

Yehova anauzira Solomo kulemba kuti: “Uteteze mtima wako kuposa zonse zimene ziyenera kutetezedwa.” (Miy 4:23) Koma n’zomvetsa chisoni kuti Aisiraeli omwe anali anthu a Mulungu anasiya kutumikira Yehova “ndi mtima wawo wonse.” (2Mb 6:14) Ngakhale Mfumu Solomo inalola kuti akazi omwe sankalambira Yehova apotoze mtima wake n’kuyamba kulambira milungu ina. (1Mf 11:4) Kodi tingateteze bwanji mtima wathu? Nkhaniyi ili mu Nsanja ya Olonda yophunzira ya January 2019, tsamba 14-19.

ONERANI VIDIYO YAKUTI ZIMENE TINAPHUNZIRA MU NSANJA YA OLONDA​—KODI TINGATETEZE BWANJI MTIMA WATHU?, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

Kodi n’chiyani chimene chikanafooketsa chikhulupiriro cha Akhristuwa, nanga nkhani yophunzirayi inawathandiza bwanji kuteteza mtima wawo?

  • Brent and Lauren

    Chithunzi cha muvidiyo yakuti “Zimene Tinaphunzira mu Nsanja ya Olonda​—Kodi Tingateteze Bwanji Mtima Wathu?” Brent ndi Lauren akufotokoza zimene zinawachitikira.
  • Umjay

    Chithunzi cha muvidiyo yakuti “Zimene Tinaphunzira mu Nsanja ya Olonda​—Kodi Tingateteze Bwanji Mtima Wathu?” Umjay akuona zithunzi za malo enaake.
  • Happy Layou

    Chithunzi cha muvidiyo yakuti “Zimene Tinaphunzira mu Nsanja ya Olonda​—Kodi Tingateteze Bwanji Mtima Wathu?” Happy akufotokoza zimene zinamuchitikira.

Kodi nkhani yophunzira imeneyi inakuthandizani bwanji?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani