CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Muzitsatira Malangizo Anzeru
Rehobowamu anafunika kusankha zochita (2Mb 10:1-4; w18-CN.06 13:3)
Rehobowamu anafunsira malangizo (2Mb 10:6-11; w01-CN 9/1 28-29)
Rehobowamu ndi anthu ena anakumana ndi mavuto chifukwa iye sanatsatire malangizo anzeru (2Mb 10:12-16; it-2 768:1)
Chifukwa cha luso komanso msinkhu wawo, Akhristu olimba mwauzimu nthawi zina akhoza kudziwiratu mmene zinthu zingathere.—Yob 12:12.
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndi ndani mumpingo amene angandipatse malangizo abwino?’