Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.11 5
  • Musamasiye Akhristu Anzanu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Musamasiye Akhristu Anzanu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • “Yembekezera Yehova”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2022
  • Kodi Yobu Anali Ndani?
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.11 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Musamasiye Akhristu Anzanu

Abale ake a Yobu anasiya kuchita naye zinthu (Yob 19:13)

Anyamata ang’onoang’ono komanso antchito ake anasiya kumulemekeza (Yob 19:​16, 18)

Anzake apamtima anamutembenukira (Yob 19:19)

Mwamuna ndi mkazi wake akuthandiza mlongo amene akukumana ndi mavuto. Mkaziyo akumvetsera mwatcheru pamene mlongoyo akulankhula ndipo mwamuna wake akukonza sinki ya ku khitchini.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingatani kuti ndipitirize kusonyeza chikondi kwa Mkhristu mnzanga amene akukumana ndi mavuto?’—Miy 17:17; w22.01 16 ¶9; w21.09 30 ¶16; w90 9/1 22 ¶20.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani