Mawu a M'munsi Zikuoneka kuti uchi umenewu sunali wa njuchi koma anali madzi azipatso, chifukwa ukutchulidwa kuti zipatso zoyambirira. (Le 2:12; 2Mb 31:5)