Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano

Mawu a M'munsi

b Imfa ya Nthumbi ya Khanda, (Sudden Infant Death Syndrome [SIDS]), imene imachitika kaŵirikaŵiri kwa makanda a mwezi umodzi mpaka miyezi isanu ndi umodzi, ndiwo mawu amene amagwiritsiridwa ntchito pamene makanda athanzi amwalira mwadzidzidzi popanda chochititsa chodziŵika bwino. M’zochitika zina, pali chikhulupiriro chakuti imfayo ingapeŵedwe ngati khandalo ligonekedwa chagada kapena cham’mbali koma osati chafufumimba. Komabe, palibe kagonekedwe kalikonse kamene kadzachinjiriza mtundu uliwonse wa imfa ya SIDS.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani