Mawu a M'munsi
c Patapita nthawi, Paulo anasankhidwa kukhala “mtumwi wotumidwa kwa anthu a mitundu ina,” koma sanali m’gulu la atumwi 12 aja. (Aroma 11:13; 1 Akor. 15:4-8) Iye sanayenerere kulandira mwayi wapadera wokhala m’gulu la atumwi 12 amenewo chifukwa sanayende ndi Yesu pa utumiki wake padziko lapansi.